Loading Events

« All Events

  • This event has passed.

Msokhano wa chitsitsimutso- Bangula akhale wa Yesu

June 15 @ 5:30 pm - June 28 @ 7:30 pm

MITU YA TSIKU NDI TSIKU
I. BUKU LOPATSA MOYO
2. UFUMU WATSOPANO WA DZIKO LAPANSI
3. ZIZINDIKIRO ZA KUBWERA KWA MFUMU
4. YANKHO KU MABVUTO A DZIKO LAPANSI
5. KODI KULI MOYO KUSELI KWA IMFA?
6. CHIZINDIKIRO CHA MULUNGU
7. BANJA LOKONDWA
8. M’MENE TINGAKHALIRE A THANZI
9, CHIYAMBI CHA MOYO WATSOPANO
10. CHINSINSI CHA CHUMA CHOKHALITSA
II. KUDZILETSA
12. YESU LOYA WATHU
13. LEMBA LA CHIROMBO
14. FUNSO LA MAFUNSO

Details

Start:
June 15 @ 5:30 pm
End:
June 28 @ 7:30 pm
Event Category:

Organizer

Pastor Katsekela

Venue

Bwalo la Ndege- Bangula trading centre
Malawi + Google Map